2 Akorinto 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Mulungu ndiye anati: “Kuwala kuunike kuchokera mu mdima,”+ ndipo kudzera mwa nkhope ya Khristu,+ waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudzana ndi kudziwa+ Mulungu. 2 Atesalonika 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anakuitanani ku chipulumutso chimenechi kudzera mu uthenga wabwino umene tikulengeza,+ kuti mudzapeze ulemerero wa Ambuye wathu Yesu Khristu.+
6 Pakuti Mulungu ndiye anati: “Kuwala kuunike kuchokera mu mdima,”+ ndipo kudzera mwa nkhope ya Khristu,+ waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudzana ndi kudziwa+ Mulungu.
14 Anakuitanani ku chipulumutso chimenechi kudzera mu uthenga wabwino umene tikulengeza,+ kuti mudzapeze ulemerero wa Ambuye wathu Yesu Khristu.+