Numeri 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano Yehova anatsegula maso a Balamu,+ ndipo iye anaona mngelo wa Yehova ali chilili panjirapo, lupanga lili m’manja. Nthawi yomweyo, Balamu anagwada pansi n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi. Numeri 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anaphanso mafumu asanu achimidiyani.+ Mafumuwo anali Evi, Rekemu, Zuri, Hura ndi Reba. Komanso anapha Balamu+ mwana wa Beori ndi lupanga.
31 Tsopano Yehova anatsegula maso a Balamu,+ ndipo iye anaona mngelo wa Yehova ali chilili panjirapo, lupanga lili m’manja. Nthawi yomweyo, Balamu anagwada pansi n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.
8 Anaphanso mafumu asanu achimidiyani.+ Mafumuwo anali Evi, Rekemu, Zuri, Hura ndi Reba. Komanso anapha Balamu+ mwana wa Beori ndi lupanga.