Yohane 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma adzachita zimenezi chifukwa sanadziwe Atate kapena ine.+ Yohane 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atate wolungama,+ ndithudi dziko silinakudziweni,+ koma ine ndikukudziwani ndipo awa adziwa kuti inu munandituma.+
25 Atate wolungama,+ ndithudi dziko silinakudziweni,+ koma ine ndikukudziwani ndipo awa adziwa kuti inu munandituma.+