Deuteronomo 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumtima mwako ukanena kuti: “Tidzadziwa bwanji kuti si Yehova amene walankhula mawuwo?”+ 2 Atesalonika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti musafulumire kugwedezeka pa maganizo anu, kapena kutengekatengeka ndi mawu ouziridwa+ onena kuti tsiku la Yehova lafika.+ Musatero ayi, ngakhale utakhala uthenga wapakamwa,+ kapena kalata+ yooneka ngati yachokera kwa ife. 1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+
2 kuti musafulumire kugwedezeka pa maganizo anu, kapena kutengekatengeka ndi mawu ouziridwa+ onena kuti tsiku la Yehova lafika.+ Musatero ayi, ngakhale utakhala uthenga wapakamwa,+ kapena kalata+ yooneka ngati yachokera kwa ife.
4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+