Mateyu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+ Chivumbulutso 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa+ ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu+ a dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitsire pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu+ la Mulungu Wamphamvuyonse.+
24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+
14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa+ ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu+ a dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitsire pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu+ la Mulungu Wamphamvuyonse.+