1 Yohane 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tikudziwa kuti tinachokera kwa Mulungu,+ koma dziko lonse lili m’manja mwa woipayo.+