Aroma 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu akuonetsa chikondi chake+ kwa ife, moti pamene tinali ochimwa, Khristu anatifera.+