Mateyu 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi nawenso sukanam’chitira chifundo+ kapolo mnzako, monga momwe ine ndinakuchitira chifundo?’+ Yohane 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Lamulo langa ndi ili, mukondane monga mmene inenso ndakukonderani.+ Aroma 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+ 1 Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tadziwa chikondi+ chifukwa chakuti iye anapereka moyo wake chifukwa cha ife,+ ndipo ifenso tiyenera kupereka moyo wathu chifukwa cha abale athu.+
8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+
16 Tadziwa chikondi+ chifukwa chakuti iye anapereka moyo wake chifukwa cha ife,+ ndipo ifenso tiyenera kupereka moyo wathu chifukwa cha abale athu.+