Yohane 6:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Munthu wakudya mnofu wanga ndi kumwa magazi anga, iyeyo ndi ine timakhala ogwirizana.+ Yohane 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+
4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+