Yohane 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene ali ndi malamulo anga ndipo amawasunga, ameneyo ndiye amene amandikonda.+ Komanso wondikonda ine, Atate wanga adzamukondanso. Inenso ndidzamukonda ndipo ndidzadzionetsera bwinobwino kwa iye.”
21 Amene ali ndi malamulo anga ndipo amawasunga, ameneyo ndiye amene amandikonda.+ Komanso wondikonda ine, Atate wanga adzamukondanso. Inenso ndidzamukonda ndipo ndidzadzionetsera bwinobwino kwa iye.”