Yohane 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana.+ Yohane 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Lamulo langa ndi ili, mukondane monga mmene inenso ndakukonderani.+ 1 Petulo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koposa zonse, khalani okondana kwambiri,+ pakuti chikondi chimakwirira machimo ochuluka.+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana.+