1 Petulo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+ 1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+
22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+
17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+