Machitidwe 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anamva chisoni kwambiri, makamaka chifukwa cha mawu amene iye ananena akuti sadzaonanso nkhope yake.+ Kenako anamuperekeza+ kukakwera ngalawa. Tito 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zena, wodziwa Chilamulo uja, komanso Apolo, uwapatse zofunika zokwanira zapaulendo, kuti asasowe kanthu.+
38 Iwo anamva chisoni kwambiri, makamaka chifukwa cha mawu amene iye ananena akuti sadzaonanso nkhope yake.+ Kenako anamuperekeza+ kukakwera ngalawa.
13 Zena, wodziwa Chilamulo uja, komanso Apolo, uwapatse zofunika zokwanira zapaulendo, kuti asasowe kanthu.+