Yakobo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumapempha koma simulandira, chifukwa mukupempha ndi cholinga choipa,+ kuti mukhutiritse zilakolako za matupi anu.+ 2 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti amalankhula mawu odzitukumula opanda pake, ndipo pogwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso makhalidwe otayirira, amakopa+ amene akungopulumuka+ kumene kwa anthu ochita zolakwa.
3 Mumapempha koma simulandira, chifukwa mukupempha ndi cholinga choipa,+ kuti mukhutiritse zilakolako za matupi anu.+
18 Pakuti amalankhula mawu odzitukumula opanda pake, ndipo pogwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso makhalidwe otayirira, amakopa+ amene akungopulumuka+ kumene kwa anthu ochita zolakwa.