Aroma 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 N’zoonadi! Iwo anadulidwa chifukwa chakuti analibe chikhulupiriro,+ koma iweyo waimirira chifukwa cha chikhulupiriro.+ Taya maganizo odzikuzawo,+ koma khala ndi mantha.+ Aheberi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho, tikuona kuti sakanatha kulowa mu mpumulowo chifukwa anali opanda chikhulupiriro.+ 1 Yohane 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wokhulupirira Mwana wa Mulungu ndiye kuti walandira umboni+ umene wapatsidwa. Munthu wosakhulupirira Mulungu ndiye kuti akumuona ngati wonama,+ chifukwa sanakhulupirire kuti zimene Mulungu wanena+ zokhudza Mwana wake, ndi zoona.+
20 N’zoonadi! Iwo anadulidwa chifukwa chakuti analibe chikhulupiriro,+ koma iweyo waimirira chifukwa cha chikhulupiriro.+ Taya maganizo odzikuzawo,+ koma khala ndi mantha.+
10 Munthu wokhulupirira Mwana wa Mulungu ndiye kuti walandira umboni+ umene wapatsidwa. Munthu wosakhulupirira Mulungu ndiye kuti akumuona ngati wonama,+ chifukwa sanakhulupirire kuti zimene Mulungu wanena+ zokhudza Mwana wake, ndi zoona.+