Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense wopitiriza kupsera mtima+ m’bale wake wapalamula mlandu+ wa kukhoti. Komano aliyense wonenera m’bale wake mawu achipongwe wapalamula mlandu wa ku Khoti Lalikulu. Ndipo aliyense wonena mnzake kuti, ‘Chitsiru iwe!’ adzapita ku Gehena* wamoto.+

  • Mateyu 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komanso ngati diso lako limakupunthwitsa ulikolowole n’kulitaya. Ndi bwino kuti ukapeze moyo uli ndi diso limodzi kusiyana ndi kuti ukaponyedwe mu Gehena* wamoto uli ndi maso onse awiri.+

  • Yakobo 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena