Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+

  • Aheberi 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+

  • Chivumbulutso 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ali ndi makutu amve+ zimene mzimu+ ukunena ku mipingo kuti: Wopambana pa nkhondo,+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+

  • Chivumbulutso 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena