Mateyu 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mayina a atumwi 12+ aja ndi awa:+ Simoni, wotchedwa Petulo,*+ ndi Andireya+ m’bale wake. Yakobo mwana wa Zebedayo+ ndi m’bale wake Yohane. Luka 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kutacha, anaitana ophunzira ake ndi kusankha 12 pakati pawo. Amenewa anawatcha “atumwi.”+ Machitidwe 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+ Aefeso 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+
2 Mayina a atumwi 12+ aja ndi awa:+ Simoni, wotchedwa Petulo,*+ ndi Andireya+ m’bale wake. Yakobo mwana wa Zebedayo+ ndi m’bale wake Yohane.
13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+
20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+