Ekisodo 39:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mzere wachiwiri+ unali ndi miyala ya nofeki, safiro+ ndi yasipi.+ Yobu 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’miyala yake mumapezeka miyala ya safiro,+Ndipo dzikolo lili ndi fumbi la golide.