Ekisodo 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uikepo miyala ndipo ikhale m’mizere inayi.+ Mzere woyamba ukhale ndi miyala ya rube,+ topazi+ ndi emarodi.+ Chivumbulutso 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wokhala pampandoyo, anali wooneka+ ngati mwala wa yasipi,+ ndi mwala wofiira wamtengo wapatali. Utawaleza+ wooneka ngati mwala wa emarodi+ unazungulira mpando wachifumuwo.
17 Uikepo miyala ndipo ikhale m’mizere inayi.+ Mzere woyamba ukhale ndi miyala ya rube,+ topazi+ ndi emarodi.+
3 Wokhala pampandoyo, anali wooneka+ ngati mwala wa yasipi,+ ndi mwala wofiira wamtengo wapatali. Utawaleza+ wooneka ngati mwala wa emarodi+ unazungulira mpando wachifumuwo.