Ekisodo 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mzere wachitatu ukhale ndi miyala ya lesemu, sibu+ ndi ametusito.+ Ekisodo 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mzere wachitatu+ unali ndi miyala ya lesemu, sibu ndi ametusito.