Yesaya 60:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dzuwa lako silidzalowanso, ndipo mwezi wako sudzapitanso kumdima. Pakuti kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+
20 Dzuwa lako silidzalowanso, ndipo mwezi wako sudzapitanso kumdima. Pakuti kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+