1 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+ Agalatiya 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kaduka, kumwa mwauchidakwa,*+ maphwando aphokoso, ndi zina zotero. Ponena za zinthu zimenezi, ndikukuchenjezeranitu, ngati mmene ndinachitira poyamba paja, kuti anthu amene amachita zimenezi+ sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+
21 kaduka, kumwa mwauchidakwa,*+ maphwando aphokoso, ndi zina zotero. Ponena za zinthu zimenezi, ndikukuchenjezeranitu, ngati mmene ndinachitira poyamba paja, kuti anthu amene amachita zimenezi+ sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+