Zekariya 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu adzakhala mumzindawo ndipo simudzakhalanso zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Anthu okhala mu Yerusalemu, adzakhala mmenemo ali otetezeka.+
11 Anthu adzakhala mumzindawo ndipo simudzakhalanso zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Anthu okhala mu Yerusalemu, adzakhala mmenemo ali otetezeka.+