Salimo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ine ndidzaona nkhope yanu m’chilungamo.+Podzuka, ndidzakhutira pokuonani.+ Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+