Aroma 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mulungu amene amapatsa mtendere+ aphwanya Satana+ pansi pa mapazi anu posachedwapa. Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu kukhale ndi inu.+ 2 Atesalonika 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kukoma mtima kwakukulu+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu kukhale nanu nonsenu.
20 Mulungu amene amapatsa mtendere+ aphwanya Satana+ pansi pa mapazi anu posachedwapa. Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu kukhale ndi inu.+