1 Akorinto 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 pakuti khomo lalikulu la mwayi wautumiki landitsegukira,+ koma pali otsutsa ambiri. 2 Akorinto 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nditafika ku Torowa+ kukalengeza uthenga wabwino wonena za Khristu, ndipo mwayi wina utanditsegukira mu ntchito ya Ambuye,+
12 Nditafika ku Torowa+ kukalengeza uthenga wabwino wonena za Khristu, ndipo mwayi wina utanditsegukira mu ntchito ya Ambuye,+