Ekisodo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.” Luka 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ndikuchita nanu pangano,+ mmene Atate wanga wachitira pangano la ufumu ndi ine,+
6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.”