Chivumbulutso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera,+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pang’ono, kufikira chitakwanira chiwerengero cha akapolo anzawo, ndi abale awo amene anali pafupi kuphedwa+ monga mmene iwonso anaphedwera. Chivumbulutso 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+
11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera,+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pang’ono, kufikira chitakwanira chiwerengero cha akapolo anzawo, ndi abale awo amene anali pafupi kuphedwa+ monga mmene iwonso anaphedwera.
8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+