Yobu 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chimafunafuna chakudya kuchokera pamenepo.+Maso ake amaona kutali kwambiri. Ezekieli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ponena za maonekedwe a nkhope zawo, zamoyo zinayi zimenezi zinali ndi nkhope ya munthu,+ nkhope ya mkango+ mbali ya kumanja,+ nkhope ya ng’ombe yamphongo+ mbali ya kumanzere,+ ndiponso nkhope ya chiwombankhanga.+
10 Ponena za maonekedwe a nkhope zawo, zamoyo zinayi zimenezi zinali ndi nkhope ya munthu,+ nkhope ya mkango+ mbali ya kumanja,+ nkhope ya ng’ombe yamphongo+ mbali ya kumanzere,+ ndiponso nkhope ya chiwombankhanga.+