Mateyu 24:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Kunena za tsikulo ndi ola lake,+ palibe amene akudziwa, ngakhale angelo akumwamba kapenanso Mwana, koma Atate yekha.+ Machitidwe 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+
36 “Kunena za tsikulo ndi ola lake,+ palibe amene akudziwa, ngakhale angelo akumwamba kapenanso Mwana, koma Atate yekha.+
7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+