Yohane 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atalandira vinyo wowawasayo, Yesu anati: “Ndakwaniritsa chifuniro chanu!”+ ndipo anaweramitsa mutu, ndi kupereka mzimu wake.+ Chivumbulutso 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anali kunena mofuula kuti: “Mwanawankhosa amene anaphedwa+ ndiye woyenera kulandira mphamvu, chuma, nzeru, nyonga, ulemu, ulemerero, ndi madalitso.”+
30 Atalandira vinyo wowawasayo, Yesu anati: “Ndakwaniritsa chifuniro chanu!”+ ndipo anaweramitsa mutu, ndi kupereka mzimu wake.+
12 Iwo anali kunena mofuula kuti: “Mwanawankhosa amene anaphedwa+ ndiye woyenera kulandira mphamvu, chuma, nzeru, nyonga, ulemu, ulemerero, ndi madalitso.”+