Salimo 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu wakhala mfumu ya mitundu ya anthu.+Mulungu wakhala pampando wake wachifumu wopatulika.+ Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+
6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+