Yesaya 48:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba.+ Ndinenso womaliza.+ Chivumbulutso 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anandiuzanso kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega, chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense womva ludzu, ndidzamupatsa madzi a m’kasupe wa moyo kwaulere.+ Chivumbulutso 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndine Alefa ndi Omega,+ woyamba ndi wotsiriza, chiyambi ndi mapeto.+
12 “Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba.+ Ndinenso womaliza.+
6 Anandiuzanso kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega, chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense womva ludzu, ndidzamupatsa madzi a m’kasupe wa moyo kwaulere.+