Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+

  • Aheberi 10:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Nthawi zina munali kupirira potonzedwa ndi posautsidwa poyera ngati chionetsero m’bwalo la masewera.+ Ndipo nthawi zina munali kupirira pamene munamva zowawa limodzi ndi ena amene anali kukumana ndi zimenezo.+

  • Chivumbulutso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena