Genesis 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Isakara+ ndi bulu wa mafupa olimba, amagona pansi atasenza matumba a katundu uku ndi uku.