Mateyu 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti pa nthawiyo kudzakhala chisautso chachikulu+ chimene sichinachitikepo kuchokera pa chiyambi cha dziko mpaka tsopano,+ ndipo sichidzachitikanso. Maliko 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti masiku amenewo adzakhala masiku a chisautso+ chimene sichinachitikepo kuchokera pa chiyambi cha chilengedwe chimene Mulungu analenga kudzafika nthawi imeneyo, ndipo sichidzachitikanso.+
21 Pakuti pa nthawiyo kudzakhala chisautso chachikulu+ chimene sichinachitikepo kuchokera pa chiyambi cha dziko mpaka tsopano,+ ndipo sichidzachitikanso.
19 Pakuti masiku amenewo adzakhala masiku a chisautso+ chimene sichinachitikepo kuchokera pa chiyambi cha chilengedwe chimene Mulungu analenga kudzafika nthawi imeneyo, ndipo sichidzachitikanso.+