1 Akorinto 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu adzakulimbitsani+ mpaka pa mapeto, kuti musakhale ndi chifukwa chokunenezerani+ m’tsiku+ la Ambuye wathu Yesu Khristu.+ 1 Akorinto 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 mupereke munthu ameneyu kwa Satana+ kuti thupilo liwonongedwe, n’cholinga choti mzimuwo+ upulumutsidwe m’tsiku la Ambuye.+
8 Mulungu adzakulimbitsani+ mpaka pa mapeto, kuti musakhale ndi chifukwa chokunenezerani+ m’tsiku+ la Ambuye wathu Yesu Khristu.+
5 mupereke munthu ameneyu kwa Satana+ kuti thupilo liwonongedwe, n’cholinga choti mzimuwo+ upulumutsidwe m’tsiku la Ambuye.+