Ekisodo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthawi yomweyo, Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba, ndipo m’dziko lonse la Iguputo munachita mdima wandiweyani kwa masiku atatu.+
22 Nthawi yomweyo, Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba, ndipo m’dziko lonse la Iguputo munachita mdima wandiweyani kwa masiku atatu.+