1Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu mwa chifuniro cha Mulungu,+ ndikulembera oyera amene ali ku Efeso, okhulupirikawo+ okhala mogwirizana+ ndi Khristu Yesu, kuti:
2“Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Efeso,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena wonyamula nyenyezi 7+ m’dzanja lake lamanja, woyenda pakati pa zoikapo nyale 7 zagolide.+