Ekisodo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukapitiriza kukaniza anthu anga kupita, mawa ndikutumizira dzombe m’dziko lako.+ Ekisodo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula+ dzanja lako ndi kuloza dziko la Iguputo, kuti dzombe ligwe m’dziko lonselo ndi kudya zomera zonse za m’dzikomo, chilichonse chimene matalala anasiya.”+
12 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula+ dzanja lako ndi kuloza dziko la Iguputo, kuti dzombe ligwe m’dziko lonselo ndi kudya zomera zonse za m’dzikomo, chilichonse chimene matalala anasiya.”+