Yoweli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Mtundu wa anthuwo umaoneka ngati mahatchi,* ndipo amathamanga ngati mahatchi amphamvu.+