Agalatiya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 inuyo simunanyansidwe ndi matenda anga, amene anali mayesero kwa inu, ndipo simunalavule malovu ponyansidwa nawo, koma munandilandira ngati mngelo+ wa Mulungu, ngati Khristu Yesu.+
14 inuyo simunanyansidwe ndi matenda anga, amene anali mayesero kwa inu, ndipo simunalavule malovu ponyansidwa nawo, koma munandilandira ngati mngelo+ wa Mulungu, ngati Khristu Yesu.+