Genesis 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Dzina la mtsinje wachitatu ndi Hidekeli,+ umene umalowera kum’mawa kwa Asuri.+ Ndipo mtsinje wachinayi ndi Firate.+ Chivumbulutso 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe. Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+
14 Dzina la mtsinje wachitatu ndi Hidekeli,+ umene umalowera kum’mawa kwa Asuri.+ Ndipo mtsinje wachinayi ndi Firate.+
12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.
15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+