Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa tsiku lachitatu kutacha, kunayamba kuchita mabingu ndi mphezi.+ Mtambo wakuda+ unakuta phiri, ndipo kunamveka kulira kwamphamvu kwambiri kwa lipenga la nyanga ya nkhosa,+ moti anthu onse mumsasawo anayamba kunjenjemera.+

  • Chivumbulutso 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kumpando wachifumuko kunali kutuluka mphezi,+ mawu, ndi mabingu.+ Panalinso nyale+ zamoto 7 zikuyaka patsogolo pa mpando wachifumuwo. Zimenezo zikuimira mizimu 7+ ya Mulungu.

  • Chivumbulutso 11:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nyumba yopatulika ya pakachisi wa Mulungu imene ili kumwamba+ inatsegulidwa, ndipo likasa+ la pangano lake linaonekera m’nyumba yake yopatulika+ ya pakachisi. Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, kunagunda mabingu, kunachita chivomezi, ndipo kunagwa matalala ambiri zedi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena