Chivumbulutso 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Sade, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena iye amene ali ndi mizimu 7+ ya Mulungu, ndi nyenyezi 7.+ ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti uli ndi dzina lakuti uli moyo, pamene ndiwe wakufa.+
3 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Sade, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena iye amene ali ndi mizimu 7+ ya Mulungu, ndi nyenyezi 7.+ ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti uli ndi dzina lakuti uli moyo, pamene ndiwe wakufa.+