Akolose 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ ku mpingo wa Alaodikaya, ndiponso mukawerenge yochokera ku Laodikaya. Chivumbulutso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+
16 Ndipo kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ ku mpingo wa Alaodikaya, ndiponso mukawerenge yochokera ku Laodikaya.
14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+