Zekariya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo iye anandiuza kuti: “Zinthu zimenezi zikuimira odzozedwa awiri+ amene amaimirira kumbali iyi ndi mbali inayi ya Ambuye wa dziko lonse lapansi.”+
14 Ndipo iye anandiuza kuti: “Zinthu zimenezi zikuimira odzozedwa awiri+ amene amaimirira kumbali iyi ndi mbali inayi ya Ambuye wa dziko lonse lapansi.”+