13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga+ wa m’mbali mwa nyanja.
Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka m’nyanja.+ Chinali ndi nyanga 10+ ndi mitu 7.+ Kunyanga yake iliyonse kunali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu.+