Chivumbulutso 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsoka limodzilo linapita. Koma masoka ena awiri+ anali kubwera pambuyo pa zimenezi.